Yeremiya 51:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tulukani mʼBabulo nʼkuthawa,Ndipo pulumutsani moyo wanu.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake. Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere. Mulungu akubwezera Babulo chifukwa cha zimene anachita.+ Zekariya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Bwera Ziyoni! Thawa iwe amene ukukhala ndi mwana wamkazi wa Babulo.*+
6 Tulukani mʼBabulo nʼkuthawa,Ndipo pulumutsani moyo wanu.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake. Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere. Mulungu akubwezera Babulo chifukwa cha zimene anachita.+