Yeremiya 50:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Lupanga lidzawononga anthu amene amalankhula zinthu zopanda pake.* Anthu amenewo adzachita zinthu mopanda nzeru. Lupanga lidzawononga asilikali a mʼBabulo, moti adzachita mantha kwambiri.+
36 Lupanga lidzawononga anthu amene amalankhula zinthu zopanda pake.* Anthu amenewo adzachita zinthu mopanda nzeru. Lupanga lidzawononga asilikali a mʼBabulo, moti adzachita mantha kwambiri.+