Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yeremiya 50:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mufuulireni mfuu yankhondo kuchokera kumbali zonse.

      Iye wavomereza kuti wagonja.*

      Zipilala zake zagwa, mipanda yake yagwetsedwa,+

      Chifukwa Yehova akumubwezera.+

      Inunso mubwezereni.

      Muchitireni zimene iye anakuchitirani.+

  • Yeremiya 51:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Ndidzalanga Beli+ ku Babulo,

      Ndipo ndidzamulavulitsa zimene wameza.+

      Mitundu ya anthu sidzapitanso kwa iye,

      Ndipo mpanda wa Babulo udzagwa.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani