-
Nehemiya 9:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Inu mwachita zinthu molungama pa zonse zimene zatichitikira. Mwachita zinthu mokhulupirika koma ife ndi amene tachita zinthu zoipa.+
-
-
Danieli 9:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ife tachimwa, tachita zinthu zolakwika komanso zoipa ndipo takupandukirani.+ Tapatuka nʼkusiya kutsatira malamulo ndi zigamulo zanu.
-
-
Danieli 9:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Inu Yehova, tachita zinthu zochititsa manyazi,* mofanana ndi mafumu athu, akalonga athu ndi makolo athu chifukwa takuchimwirani.
-