Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 31:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pa nthawi imeneyo mkwiyo wanga udzawayakira+ ndipo ndidzawasiya+ nʼkuwabisira nkhope yanga+ mpaka atawonongedwa.+ Ndiyeno akadzakumana ndi masoka komanso mavuto ambiri adzanena kuti, ‘Masoka amenewatu akutigwera chifukwa chakuti Mulungu wathu sali pakati pathu.’+

  • Yesaya 27:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tinthambi take tikadzauma,

      Akazi adzabwera kudzatithyola

      Nʼkukakolezera moto.

      Anthu awa samvetsa zinthu,+

      Nʼchifukwa chake amene anawapanga sadzawachitira chifundo,

      Ndipo amene anawaumba sadzawakomera mtima.+

  • Yesaya 63:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma iwo anapanduka+ nʼkumvetsa chisoni mzimu wake woyera.+

      Kenako iye anakhala mdani wawo,+

      Ndipo anachita nawo nkhondo.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani