-
Yeremiya 23:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Kodi maganizo onena zabodza apitiriza kukhala mumtima mwa aneneriwa mpaka liti? Iwo ndi aneneri amene amanena chinyengo chochokera mumtima mwawo.+
-