Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yeremiya 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndidzawasandutsa chinthu chochititsa mantha kwa maufumu onse apadziko lapansi,+ chifukwa cha zimene Manase mwana wa Hezekiya, mfumu ya Yuda, anachita mu Yerusalemu.+

  • Yeremiya 34:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho Yehova wanena kuti, ‘Inu simunamvere mawu anga oti mulengeze ufulu, aliyense kwa mʼbale wake ndi kwa mnzake.+ Tsopano ine ndikulengeza ufulu kwa inu,’ akutero Yehova. ‘Inu mudzafa ndi lupanga, mliri* ndi njala.+ Ndidzakusandutsani chinthu chimene maufumu onse apadziko lapansi adzachita nacho mantha.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani