-
Ezekieli 39:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 ‘Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo, ndikadzawapititsa ku ukapolo pakati pa anthu a mitundu ina, kenako nʼkuwabwezeretsa kudziko lawo osasiyako wina aliyense.+
-