Yesaya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Malo olowera mumzinda adzalira ndipo adzamva chisoni,+Mzindawo udzakhala padothi penipeni ndipo udzakhala wopanda chilichonse.”+
26 Malo olowera mumzinda adzalira ndipo adzamva chisoni,+Mzindawo udzakhala padothi penipeni ndipo udzakhala wopanda chilichonse.”+