Yeremiya 29:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Ine ndikuwatumizira lupanga, njala ndi mliri*+ ndipo ndidzawachititsa kuti akhale ngati nkhuyu zowola* zimene ndi zoipa kwambiri moti munthu sangadye.”’+ Yeremiya 38:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova wanena kuti, ‘Amene atsale mumzinda uno adzafa ndi lupanga, njala ndi mliri.*+ Koma amene adzadzipereke* kwa Akasidi adzapitiriza kukhala ndi moyo. Adzapulumutsa moyo wake, sadzafa ayi.’+
17 ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Ine ndikuwatumizira lupanga, njala ndi mliri*+ ndipo ndidzawachititsa kuti akhale ngati nkhuyu zowola* zimene ndi zoipa kwambiri moti munthu sangadye.”’+
2 “Yehova wanena kuti, ‘Amene atsale mumzinda uno adzafa ndi lupanga, njala ndi mliri.*+ Koma amene adzadzipereke* kwa Akasidi adzapitiriza kukhala ndi moyo. Adzapulumutsa moyo wake, sadzafa ayi.’+