-
Salimo 107:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Chifukwa anapandukira mawu a Mulungu,
Ananyoza malangizo a Wamʼmwambamwamba.+
-
-
Yesaya 1:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Imvani inu okhala kumwamba, ndipo tcherani khutu inu okhala padziko lapansi,+
Chifukwa Yehova wanena kuti:
-