Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 8:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa+ tili ngati zizindikiro+ ndiponso ngati zodabwitsa mu Isiraeli, zochokera kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, amene amakhala mʼphiri la Ziyoni.

  • Ezekieli 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Utenge chiwaya ndipo uchiike pakati pa iweyo ndi mzindawo kuti chikhale ngati khoma lachitsulo. Uziyangʼana mzindawo monyansidwa ndipo usonyeze zimene adani adzachite poukira mzindawo. Chimenechi chikhale chizindikiro ku mtundu wa Isiraeli.+

  • Ezekieli 24:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ezekieli wakhala chizindikiro kwa inu.+ Mudzachita zonse zimene iye wachita. Tsokali likadzakugwerani, mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”’”

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani