Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mafumu 14:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Iye adzasiya Aisiraeli chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita ndiponso amene Aisiraeli anachita chifukwa cha iyeyo.”+

  • 1 Mafumu 21:25, 26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Palibenso munthu wina amene anatsimikiza mumtima mwake kuchita zoipa pamaso pa Yehova ngati Ahabu.+ Mkazi wake Yezebeli anamulimbikitsa kuchita zimenezo.+ 26 Ahabu anachita zinthu zonyansa kwambiri polambira mafano onyansa* ngati mmene Aamori onse anachitira, amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa Aisiraeli.’”+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani