Hoseya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa mayi awo amachita uhule.*+ Mayi amene anatenga pakati nʼkuwabereka achita zinthu zochititsa manyazi+ ndipo anena kuti,‘Nditsatira amuna ondikonda kwambiri+Ndiponso amene amandipatsa chakudya ndi madzi,Amandipatsanso zovala za ubweya wa nkhosa, nsalu, mafuta ndi zakumwa.’
5 Chifukwa mayi awo amachita uhule.*+ Mayi amene anatenga pakati nʼkuwabereka achita zinthu zochititsa manyazi+ ndipo anena kuti,‘Nditsatira amuna ondikonda kwambiri+Ndiponso amene amandipatsa chakudya ndi madzi,Amandipatsanso zovala za ubweya wa nkhosa, nsalu, mafuta ndi zakumwa.’