Amosi 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wanena kuti, ‘Masiku adzafika,Pamene wolima adzapitirira wokolola,Ndipo woponda mphesa adzapitirira wonyamula mbewu.+Mʼmapiri akuluakulu mudzatuluka vinyo wotsekemera+Ndipo mʼmapiri angʼonoangʼono muzidzatuluka vinyo wambiri.+ Zekariya 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ubwino wake ndi waukulu kwambiri,+Ndiponso iye ndi wooneka bwino kwambiri. Tirigu adzapatsa mphamvu anyamata,Ndipo vinyo watsopano adzapatsa mphamvu anamwali.”+
13 Yehova wanena kuti, ‘Masiku adzafika,Pamene wolima adzapitirira wokolola,Ndipo woponda mphesa adzapitirira wonyamula mbewu.+Mʼmapiri akuluakulu mudzatuluka vinyo wotsekemera+Ndipo mʼmapiri angʼonoangʼono muzidzatuluka vinyo wambiri.+
17 Ubwino wake ndi waukulu kwambiri,+Ndiponso iye ndi wooneka bwino kwambiri. Tirigu adzapatsa mphamvu anyamata,Ndipo vinyo watsopano adzapatsa mphamvu anamwali.”+