Yesaya 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova adzabweretsera iweyo, anthu ako komanso nyumba ya bambo ako nthawi yovuta imene sinakhaleponso kuyambira tsiku limene Efuraimu anapatukana ndi Yuda.+ Iye adzakubweretserani mfumu ya Asuri.+
17 Yehova adzabweretsera iweyo, anthu ako komanso nyumba ya bambo ako nthawi yovuta imene sinakhaleponso kuyambira tsiku limene Efuraimu anapatukana ndi Yuda.+ Iye adzakubweretserani mfumu ya Asuri.+