Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ezekieli 27:32, 33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Polira adzaimba nyimbo yoimba polira ndipo adzakuimbira kuti:

      ‘Ndi ndani angafanane ndi Turo, amene wawonongedwa* pakati pa nyanja?+

      33 Katundu wako atabwera kuchokera pakatikati pa nyanja, unasangalatsa anthu ambiri.+

      Chuma chako chochuluka komanso malonda ako zinalemeretsa mafumu apadziko lapansi.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani