-
Ezekieli 28:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Iwe waipitsa malo ako opatulika chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zako komanso malonda ako opanda chilungamo.
Ndidzachititsa kuti moto uyake pakati pako ndipo udzakupsereza.+
Ndidzakusandutsa phulusa padziko lapansi, pamaso pa anthu onse amene akukuyangʼana.
-