Salimo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzawauza kuti: “Inetu ndasankha mfumu yanga+Ndipo ikulamulira ku Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.” Yesaya 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yeremiya 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Taonani! Masiku adzafika,” watero Yehova, “pamene ndidzaike mfumu yolungama pampando wachifumu yochokera mʼbanja lachifumu la Davide.*+ Mfumuyo idzalamulira mʼdzikoli+ ndipo idzachita zinthu mwanzeru, motsatira malamulo komanso mwachilungamo.+ Luka 19:37, 38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yohane 1:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
6 Iye adzawauza kuti: “Inetu ndasankha mfumu yanga+Ndipo ikulamulira ku Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.”
5 “Taonani! Masiku adzafika,” watero Yehova, “pamene ndidzaike mfumu yolungama pampando wachifumu yochokera mʼbanja lachifumu la Davide.*+ Mfumuyo idzalamulira mʼdzikoli+ ndipo idzachita zinthu mwanzeru, motsatira malamulo komanso mwachilungamo.+