-
Ezekieli 34:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ine ndidzapulumutsa nkhosa zanga, ndipo sizidzagwidwanso ndi zilombo.+ Ndidzaweruza pakati pa nkhosa ndi nkhosa inzake.
-