Yeremiya 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mʼmasiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Isiraeli adzakhala motetezeka.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala: Yehova Ndi Chilungamo Chathu.”+ Yeremiya 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mʼmasiku amenewo Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Yerusalemu adzakhala mwamtendere.+ Yerusalemu azidzatchulidwa kuti, Yehova Ndi Chilungamo Chathu.’”+
6 Mʼmasiku a mfumu imeneyi, Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Isiraeli adzakhala motetezeka.+ Dzina la mfumuyi lidzakhala: Yehova Ndi Chilungamo Chathu.”+
16 Mʼmasiku amenewo Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Yerusalemu adzakhala mwamtendere.+ Yerusalemu azidzatchulidwa kuti, Yehova Ndi Chilungamo Chathu.’”+