-
Ezekieli 38:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 ‘Ndidzamuyambitsira nkhondo mʼmapiri anga onse kuti amuwononge,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Aliyense adzapha mʼbale wake ndi lupanga.+
-