Salimo 86:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitundu yonse ya anthu imene munapangaIdzabwera nʼkudzagwada pamaso panu, inu Yehova,+Ndipo idzalemekeza dzina lanu.+
9 Mitundu yonse ya anthu imene munapangaIdzabwera nʼkudzagwada pamaso panu, inu Yehova,+Ndipo idzalemekeza dzina lanu.+