Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Samueli 2:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Munthu aliyense akamapereka nsembe ankayeneranso kupereka gawo la nyamayo kwa wansembe.+ Ndiyeno zimene zinkachitika nʼzakuti nyamayo ikamawira, mtumiki wa wansembe ankabwera foloko ya mano atatu ili mʼmanja. 14 Akatero ankapisa folokoyo mʼbeseni, mʼpoto wa zogwirira ziwiri, mumphika kapena mʼpoto wa chogwirira chimodzi. Ndiyeno wansembe ankatenga chilichonse chimene folokoyo yatulutsa. Zimenezi ndi zimene ankachitira Aisiraeli onse opita ku Silo.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani