Ekisodo 25:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Numeri 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo aziyalanso nsalu yabuluu patebulo la mkate wachionetsero,+ nʼkuikapo mbale, makapu, mbale zolowa ndi mitsuko ya nsembe yachakumwa.+ Mkate wachionetsero+ womwe ndi nsembe ya nthawi zonse uzikhalabe pomwepo.
7 Iwo aziyalanso nsalu yabuluu patebulo la mkate wachionetsero,+ nʼkuikapo mbale, makapu, mbale zolowa ndi mitsuko ya nsembe yachakumwa.+ Mkate wachionetsero+ womwe ndi nsembe ya nthawi zonse uzikhalabe pomwepo.