Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili M‘buku la Mika MIKA ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Chiweruzo cha Samariya ndi Yuda (1-16) Machimo ndi kugalukira zinabweretsa mavuto (5) 2 Tsoka kwa opondereza anzawo (1-11) Aisiraeli anagwirizanitsidwa (12, 13) Mʼdziko mudzadzaza phokoso la anthu (12) 3 Atsogoleri ndi aneneri anadzudzulidwa (1-12) Mika anapatsidwa mphamvu ndi mzimu wa Yehova (8) Ansembe ankaphunzitsa kuti apeze ndalama (11) Yerusalemu adzakhala bwinja (12) 4 Phiri la Yehova lidzakwezedwa (1-5) Kusula malupanga kuti akhale makasu a pulawo (3) ‘Ife tidzayenda mʼdzina la Yehova’ (5) Ziyoni adzakhalanso wamphamvu (6-13) 5 Wolamulira amene adzakhale wamphamvu padziko lonse (1-6) Wolamulira adzachokera ku Betelehemu (2) Anthu otsala adzakhala ngati mame komanso mkango (7-9) Dziko lidzayeretsedwa (10-15) 6 Mulungu anaimba mlandu Aisiraeli (1-5) Yehova akufuna kuti uzichita chiyani? (6-8) Chilungamo, kukhulupirika, kudzichepetsa (8) Aisiraeli analakwa nʼkulangidwa (9-16) 7 Makhalidwe oipa a Aisiraeli (1-6) Adani a munthu adzakhala anthu a mʼbanja lake (6) “Ine ndidzayembekezera Yehova” (7) Anthu a Mulungu zinthu zidzawayendera bwino (8-13) Mika anapemphera komanso kutamanda Mulungu (14-20) Yehova anayankha (15-17) ‘Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi Yehova?’ (18)