Magazini Yophunzia
September 2016
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA OCTOBER 24 MPAKA NOVEMBER 27, 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
FIJI
Abale ndi alongo amene amakhala kunja kwa mzinda wa Suva, womwe ndi likulu la dzikoli, amasangalala kulalikira uthenga wabwino kwa aliyense amene akumana naye
KULI ANTHU
887,027
KULI OFALITSA
3,097
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2015)
11,845
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.