Nsanja ya Olonda Yophunzira
SEPTEMBER 2017
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: OCTOBER 23–NOVEMBER 26, 2017
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
EL SALVADOR
Mabanja awiri akulalikira pogwiritsa ntchito mashelefu amatayala pafupi ndi mashopu ku San Salvador
KULI OFALITSA
41,084
MAPHUNZIRO A BAIBULO
42,813
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2016)
92,606
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.