Magazini Yophunzira
FEBRUARY 2018
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: APRIL 2-29, 2018
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
CAMBODIA
Banja la Mboni likulalikira mayi wina amene wapita kukatenga mwana wake kusukulu. Mayiyo wavala mpango umene anthu a kumeneko amaukonda
KULI OFALITSA
1,021
MAPHUNZIRO A BAIBULO
2,524
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2016)
2,790
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.