Magazini Yophunzira
SEPTEMBER 2018
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: OCTOBER 29–DECEMBER 2, 2018
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
IRELAND
Abale amapita kukalalikira kwa anthu amene amakhala kuzilumba za Aran, zomwe zili kumadzulo kwa Ireland, ndipo amawalalikira m’Chiairishi
KULI OFALITSA
6,747
MAPHUNZIRO A BAIBULO
3,392
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2017)
12,082
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka, pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.