Magazini Yophunzira
DECEMBER 2018
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: FEBRUARY 4–MARCH 3, 2019
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
MYANMAR
Alongo awiri akupeza anthu ambiri amene angawalalikire mumsika wa ku Taunggyi
OFALITSA
4,296
MAPHUNZIRO A BAIBULO
4,329
OPEZEKA PACHIKUMBUTSO (2017)
8,659
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka, pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.