Magazini Yophunzira
JANUARY 2019
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: MARCH 4–APRIL 7, 2019
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI PATSAMBA LOYAMBA:
Anthu mamiliyoni ambiri padziko lonse akuitanidwa ku Chikumbutso (Onani nkhani yophunzira 5, ndime 1-2)