Magazini Yophunzira
SEPTEMBER 2019
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: OCTOBER 28–DECEMBER 1, 2019
© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
PATSAMBA LOYAMBA:
Mtumwi Yohane anaona a “khamu lalikulu” atavala mikanjo yoyera ndiponso atanyamula nthambi zakanjedza m’manja mwawo (Onani nkhani yophunzira 39, ndime 2)