Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb17.11 6
  • Khalanibe Maso

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Khalanibe Maso
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • Muzikhulupirira Yehova Kuti Mukhale ndi Moyo
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
  • Khalanibe Maso Pamene Zinthu Zasintha
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17.11 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | NAHUMU 1–HABAKUKU 3

Khalanibe Maso

Hab. 1:5, 6

Zinali zosayembekezereka kuti Ababulo angawononge mzinda wa Yuda. Ayuda ankathandizidwa ndi Aiguputo omwe anali amphamvu kwambiri kuposa Ababulo. Kuwonjezera apo, Ayuda ambiri ankaona kuti Yehova sangalole kuti Yerusalemu ndi kachisi ziwonongedwe. Komabe ulosi unkayenera kukwaniritsidwa ndithu ndipo Habakuku ankafunika kukhalabe maso pouyembekezera.

Habakuku anakhalabe maso ngakhale kuti panali anthu ambiri amene ankachita zoipa

Kodi n’chiyani chikunditsimikizira kuti mapeto a dzikoli ali pafupi kwambiri?

Kodi ndingatani kuti ndikhalebe maso?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani