Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.01 2
  • “Ufumu Wakumwamba Wayandikira”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Ufumu Wakumwamba Wayandikira”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Yohane Anakonza Njira
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Pitirizani Kukhala Maso M’masiku Otsiriza Ano
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.01 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 1-3

“Ufumu Wakumwamba Wayandikira”

3:4

  • Yohane M’batizi

    Zovala za Yohane zinkasonyezeratu kuti ankakhala moyo wosalira zambiri komanso kuti anali wodzipereka pochita chifuniro cha Mulungu

  • Yohane anali ndi mwayi wapadera kwambiri wogwira ntchito yodziwitsa anthu za kubwera kwa Yesu

Kukhala ndi moyo wosalira zambiri kungatithandize kuti tizichita zochuluka potumikira Mulungu ndipo tingamakhale osangalala. Kuti tikhale ndi moyo wosalira zambiri tiyenera . . .

  • kuzindikira zinthu zomwe ndi zofunikadi

  • kusiya kugula zinthu zosafunika kwenikweni

  • kulemba bajeti

  • kuchotsa zinthu zimene sitizigwiritsa ntchito

  • kulipira ngongole zonse

  • kuchepetsa nthawi imene timagwira ntchito

Uchi wam’tchire komanso dzombe

Yohane ankangodya dzombe ndi uchi

Kodi ndingakwaniritse cholinga chiti ngati nditamakhala moyo wosalira zambiri?

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani