Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.02 4
  • February 12-18

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 12-18
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.02 4

February 12-18

MATEYU 14-15

  • Nyimbo Na. 93 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yesu Amadyetsa Anthu Ambiri Kudzera Mwa Anthu Ochepa”: (10 min.)

    • Mat. 14:16, 17​—Ophunzira a Yesu anali ndi mitanda 5 ya mkate ndi nsomba ziwiri (w13 7/15 15 ¶2)

    • Mat. 14:18, 19​—Yesu anadyetsa khamu lalikulu la anthu pogwiritsa ntchito ophunzira ake (w13 7/15 15 ¶3)

    • Mat. 14:20, 21​—Anthu ambirimbiri anapindula ndi chozizwitsa chimene Yesu anachita (“osawerengera akazi ndi ana aang’ono” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 14:21, nwtsty; w13 7/15 15 ¶1)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Mat. 15:7-9​—N’chifukwa chiyani tiyenera kupewa chinyengo? (“Onyenga” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 15:7, nwtsty)

    • Mat. 15:26​—Kodi n’kutheka kuti Yesu ankatanthauza chiyani pamene ananena mawu akuti “tiagalu”? (“ana . . . tiagalu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 15:26, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 15:1-20

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w15 9/15 16-17 ¶14-17​—Mutu: Tizitsatira Yesu Kuti Tilimbitse Chikhulupiriro Chathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 135

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Mmene Mungapezere Anzanu: (7 min.) Onetsani vidiyoyi. Kenako pemphani ana amene munawasankhiratu kuti abwere kupulatifomu ndipo muwafunse mafunso otsatirawa: N’chifukwa chiyani muyenera kukhala ndi anzanu amene amakonda Yehova? Kodi mungaphunzire chiyani kwa anzanu oterowo?

  • “Uzilemekeza Bambo Ako ndi Mayi Ako”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Kodi Ndingatani Kuti Ndizilankhulana Bwino ndi Makolo Anga?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 14 ¶1-7

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 148 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani