Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.07 3
  • July 9-15

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 9-15
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.07 3

July 9-15

Luka 8-9

  • Nyimbo Na. 13 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Chofunika N’chiyani Kuti Munthu Akhale Wotsatira wa Yesu?”: (10 min.)

    • Luka 9:57, 58​—Anthu amene amatsatira Yesu ayenera kumakhulupirira kwambiri Yehova (it-2 494)

    • Luka 9:59, 60​—Anthu amene amatsatira Yesu amaika Ufumu wa Mulungu pamalo oyamba pamoyo wawo (nwtsty mfundo zimene ndikuphunzira)

    • Luka 9:61, 62​—Anthu amene amatsatira Yesu samalola kuti zinthu za m’dzikoli ziwasokoneze (nwtsty zithunzi ndi mavidiyo; w12 4/15 15-16 ¶11-13)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Luka 8:3​—Kodi Akhristu amenewa ‘anatumikira’ bwanji Yesu komanso atumwi? (nwtsty mfundo zimene ndikuphunzira)

    • Luka 9:49, 50​—N’chifukwa chiyani Yesu sanaletse munthu wina kutulutsa ziwanda ngakhale kuti sanali wotsatira wake? (w08 3/15 31 ¶3)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 8:1-15

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w12 3/15 27-28 ¶11-15​—Mutu: Kodi Tiyenera Kumanong’oneza Bondo Tikaganizira Zinthu Zimene Tinasiya Chifukwa cha Ufumu wa Mulungu?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 124

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 21 ¶8-14

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 110 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani