Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.09 2
  • September 3-9

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • September 3-9
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.09 2

September 3-9

YOHANE 1-2

  • Nyimbo Na. 13 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Chozizwitsa Choyamba cha Yesu”: (10 min.)

    • [Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yohane.]

    • Yoh. 2:1-3​—Pa mwambo wina wa ukwati panachitika zinthu zomwe zikanachititsa manyazi banja latsopanolo (w15 6/15 4 ¶3)

    • Yoh. 2:4-11​—Zimene Yesu anachita zinalimbitsa chikhulupiriro cha ophunzira ake (jy 41 ¶6)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yoh. 1:1​—Kodi n’chiyani chikusonyeza kuti Yohane sankatanthauza kuti “Mawu” anali Mulungu Wamphamvuyonse? (“Mawu” “ndi” “Mawuyo anali mulungu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 1:1, nwtsty)

    • Yoh. 1:29​—N’chifukwa chiyani Yohane M’batizi anatchula Yesu kuti “Mwanawankhosa wa Mulungu”? (“Mwanawankhosa wa Mulungu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 1:29, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 1:1-18

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha wobwereza woyamba.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs tsamba 50, Mfundo 2

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 38

  • Zofunika Pampingo: (8 min.)

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onetsani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya September.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 3

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 141 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani