Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.09 4
  • September 17-23

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • September 17-23
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.09 4

September 17-23

YOHANE 5-6

  • Nyimbo Na. 2 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzitsatira Yesu Muli ndi Zolinga Zabwino”: (10 min.)

    • Yoh. 6:9-11​—Yesu anadyetsa khamu la anthu mozizwitsa (“amuna pafupifupi 5,000 anakhaladi pansi” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 6:10, nwtsty)

    • Yoh. 6:14, 24​—Anthuwo anadziwa kuti Yesu ndi Mesiya ndipo tsiku lotsatira anayamba kumufunafuna (“mneneri” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 6:14, nwtsty)

    • Yoh. 6:25-27, 54, 60, 66-69​—Popeza anthuwo ankatsatira Yesu komanso ophunzira ake ndi zolinga zolakwika, anakhumudwa ndi mawu amene iye analankhula (“chakudya chimene chimawonongeka . . . chopereka moyo wosatha” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 6:27, nwtsty; “wakudya mnofu wanga ndi kumwa magazi anga” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 6:54, nwtsty; w05 9/1 21 ¶13-14)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yoh. 6:44​—Kodi Atate amakokera bwanji anthu kwa iye? (“kukokedwa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 6:44, nwtsty)

    • Yoh. 6:64​—Kodi Yesu ankatanthauza chiyani pamene ananena kuti ankadziwa “kuchokera pa chiyambi” kuti Yudasi adzamupereka? (“Yesu anadziwa . . . amene adzamupereka” “kuchokera pa chiyambi” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 6:64, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 6:41-59

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri.

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. Sonyezani zimene mungachite ngati amene mukumulalikira wanena kuti ndi Mkhristu.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 31

  • Kodi Zinayenda Bwanji?: (5 min.) Nkhani yokambirana. Pemphani abale ndi alongo kuti afotokoze zosangalatsa zimene zinawachitikira pamene ankayesa kucheza ndi anthu kuti awalalikire.

  • “Sipanawonongeke Chilichonse”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani mbali ina ya vidiyo yakuti, Nyumba Zabwino Kwambiri Zimene Zimalemekeza Yehova.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 5

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 95 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani