Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.09 6
  • September 24-30

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • September 24-30
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.09 6

September 24-30

YOHANE 7-8

  • Nyimbo Na. 12 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yesu Ankalemekeza Atate Wake”: (10 min.)

    • Yoh. 7:15-18​—Anthu ena atamuyamikira kuti amaphunzitsa bwino, Yesu anawauza kuti zimene amaphunzitsazo zimachokera kwa Yehova (cf 100-101 ¶5-6)

    • Yoh. 7:28, 29​—Yesu ananena kuti anachita kutumidwa ndi Yehova, zomwe zikusonyeza kuti amamumvera

    • Yoh. 8:29​—Yesu anauza anthu kuti iye amachita zinthu zimene zimakondweretsa Yehova nthawi zonse (w11 3/15 11 ¶19)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yoh. 7:8-10​—Kodi pamenepa Yesu ankawanamiza abale akewo? (w07 2/1 6 ¶4)

    • Yoh. 8:58​—Kodi n’chiyani chikutitsimikizira kuti mawu amene ali kumapeto kwa vesili akuti “ine n’kuti ndilipo kale” ndi olondola, nanga n’chifukwa chiyani kudziwa zimenezi n’kofunika? (“ine n’kuti ndilipo kale” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 8:58, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 8:31-47

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. Kenako muitanireni kumisonkhano yathu.

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse ndipo gawirani buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lvs 9-10 ¶10-11

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 103

  • “Muzitsanzira Khristu pa Nkhani Yokhala Odzichepetsa Komanso Kuzindikira Malire Anu”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani mavidiyo onse.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 6, ndi bokosi lakuti “Masiku Akuti Ayeretsedwe Anakwanira”

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 138 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani