Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb18.12 3
  • December 10-16

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 10-16
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18.12 3

December 10-16

MACHITIDWE 12-14

  • Nyimbo Na. 60 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Baranaba ndi Paulo Ankathandiza Anthu Kukhala Ophunzira M’madera Akutali Kwambiri”: (10 min.)

    • Mac. 13:2, 3​—Yehova anasankha Baranaba ndi Saulo kuti agwire ntchito yapadera (bt 86 ¶4)

    • Mac. 13:12, 48; 14:1​—Ntchito yawo inathandiza kuti anthu ambiri akhale Akhristu (bt 95 ¶5)

    • Mac. 14:21, 22​—Baranaba ndi Paulo analimbikitsa ophunzira atsopanowo (w14 9/15 13 ¶4-5)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Mac. 12:21-23​—Kodi zimene zinachitikira Herode zikutiphunzitsa chiyani? (w08 5/15 32 ¶7)

    • Mac. 13:9​—N’chifukwa chiyani Saulo ‘ankatchedwanso Paulo’? (“Saulo, wotchedwanso Paulo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mac. 13:9, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mac. 12:1-17

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsirani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) bt 78-79 ¶8-9​—Mutu: Muzipempherera Okhulupirira Anzanu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 65

  • “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Muzithandiza Anthu Amene Ali ndi ‘Maganizo Abwino’ Kuti Akhale Ophunzira”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Yehova Mulungu Adzakuthandizani .

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 17

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 86 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani