Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb19.11 5
  • November 18-24

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 18-24
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19.11 5

November 18-24

CHIVUMBULUTSO 1-3

  • Nyimbo Na. 15 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Ndikudziwa Ntchito Zako”: (10 min.)

    • [Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Chivumbulutso.]

    • Chiv. 1:20​—Yesu amaona zonse zimene akulu amachita mumpingo (w12 10/15 14 ¶8)

    • Chiv. 2:1, 2​—Yesu amadziwa zimene zimachitika mumpingo uliwonse (w12 4/15 29 ¶11; w01 1/15 20-21 ¶20)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Chiv. 1:7​—Kodi diso lililonse lidzamuona bwanji Yesu “akubwera ndi mitambo,” nanga zimenezi zidzachitika liti? (kr 226 ¶10)

    • Chiv. 2:7​—Kodi “kudya za mumtengo wa moyo, umene uli m’paradaiso wa Mulungu,” kumatanthauza chiyani? (w09 1/15 31 ¶1)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Chiv. 1:1-7 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. (th phunziro 2)

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? kenako kambiranani naye mfundo za m’vidiyoyi. (th phunziro 3)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 4

  • “Yehova Amadziwa Zimene Timafunikira”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Lipoti la Komiti Yophunzitsa la 2017.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs 13:1-8

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 124 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani