Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb20.04
  • April 20-26

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 20-26
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20.04

April 20-26

GENESIS 32-33

  • Nyimbo Na. 21 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mukuyesetsa Kuchita Zonse Zomwe Mungathe Kuti Mupeze Madalitso?”: (10 min.)

    • Ge 32:24​—Yakobo analimbana ndi mngelo (w03 8/15 25 ¶3)

    • Ge 32:25, 26​—Yakobo sanagonje mpaka atalandira madalitso (it-2 190)

    • Ge 32:27, 28​—Yakobo anadalitsidwa chifukwa cha khama lake (it-1 1228)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Ge 32:11, 13-15​—Kodi tingatengere bwanji chitsanzo cha Yakobo pa nkhani yokhazikitsa mtendere? (w10 6/15 22 ¶10-11)

    • Ge 33:20​—N’chifukwa chiyani Yakobo anatchula guwa lansembeli kuti “Mulungu, Mulungu wa Isiraeli”? (it-1 980)

    • Kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ge 32:1-8 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: N’chifukwa chiyani tinganene kuti Elise ananena zolondola komanso analalikira mogwira mtima? Kodi Elise ndi Megan anathandizana bwanji kuti alalikire mogwira mtima?

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. (th phunziro 12)

  • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? kenako kambiranani naye mfundo za m’vidiyoyi. (th phunziro 16)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 35

  • “Kodi Chofunika Kwambiri kwa Ine N’chiyani?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Musasiye Kukhala ndi Zolinga Zauzimu.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia Mutu 2 ndime 1-8

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (Osapitirira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 108 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani