September 14-20
EKISODO 25-26
Nyimbo Na. 18 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Chinthu Chofunika Kwambiri M’chihema”: (10 min.)
Eks 25:9—Yehova anauza Mose mmene ayenera kupangira likasa la pangano (it-1 165)
Eks 25:21—Likasa linali chinthu choyera chosungiramo umboni wopatulika (it-1 166 ¶2)
Eks 25:22—Likasa linkaimira kukhalapo kwa Mulungu (it-1 166 ¶3)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Eks 25:20—Kodi mmene akerubi analili pachivundikiro cha Likasa n’kutheka kuti zinkasonyeza chiyani? (it-1 432 ¶1)
Eks 25:30—Kodi mkate wachionetsero unali chiyani? (it-2 936)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Eks 25:23-30 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi wofalitsayu wasonyeza bwanji chikondi komanso chifundo? Kodi iye akanachita chiyani kuti asonyeze munthuyu chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira?
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 8)
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako gawirani chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 11)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zimene Gulu Lathu Lachita: (5 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya September.
Zofunika Pampingo: (10 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) ia 8:22-27 ndi mfundo zobwereza
Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)
Nyimbo Na. 128 ndi Pemphero