January 11-17
LEVITIKO 20-21
Nyimbo Na. 80 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Amafuna Kuti Anthu Ake Azikhala Osiyana ndi Ena”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Le 20:1-8 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Ulendo Wobwereza: Pemphero—1Yo 5:14. Muziimitsa nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 6)
Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni kabuku ka Uthenga Wabwino, ndipo yambitsani phunziro pa mutu 12. (th phunziro 19)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Tetezani Banja Lanu”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Tiyenera ‘Kuthamanga Mopirira’—Muzitsatira Malamulo a Mpikisano.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia 14:17-23 ndi Mfundo Zobwereza
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 130 ndi Pemphero