Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb21.01 8
  • January 18-24

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 18-24
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21.01 8

January 18-24

LEVITIKO 22-​23

  • Nyimbo Na. 86 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zikondwerero Zomwe Zimatikhudza”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Le 22:​21, 22​—N’chifukwa chiyani tiyenera kukhala okhulupirika kwa Yehova ndi mtima wathu wonse? (w19.02 6:3)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Le 23:​9-​16 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Gawirani magazini yomwe ili ndi nkhani imene mwininyumba anatchula. (th phunziro 13)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 9)

  • Nkhani: (5 min.) w07 7/15 26​—Mutu: Kodi Ndani Ankakolola Barele Woyamba Kucha N’kupita Naye Kukachisi? (th phunziro 13)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 87

  • “Misonkhano Yachigawo Imatipatsa Mwayi Wosonyezana Chikondi”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Msonkhano Wamayiko Wakuti “Chikondi Sichitha.”

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia 15:1-9

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 49 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani