Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb21.01 11
  • January 25-31

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 25-31
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21.01 11

January 25-31

LEVITIKO 24-​25

  • Nyimbo Na. 144 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Chaka cha Ufulu Komanso Ufulu Womwe Tidzakhale Nawo M’tsogolo”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Le 24:20​—Kodi Mawu a Mulungu amaphunzitsa kuti munthu akatilakwira tizibwezera? (w09 9/1 22 ¶3)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Le 24:​1-​12 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 16)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni kapepala komuitanira kumisonkhano yathu ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? kenako kambiranani naye mfundo za m’vidiyoyi. (th phunziro 11)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) fg phunziro 12:6-7 (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 139

  • Zofunika Pampingo (5 min.)

  • “Timathokoza Mulungu ndi Khristu Chifukwa cha Ufulu Womwe Tidzakhale Nawo”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Pitirizani Kuyang’anitsitsa Yesu Pamene Mphepo Yamkuntho Ikubwera​—Madalitso Amene Ufumu Udzabweretse.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia 15:10-19

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 35 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani