Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb21.01 17
  • February 8-14

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 8-14
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21.01 17

February 8-14

NUMERI 1–2

  • Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Amachita Zinthu Mwadongosolo ndi Anthu Ake”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Nu 1:​2, 3​—N’chifukwa chiyani anthu ankalembedwa m’kaundula ku Isiraeli? (it-2 764)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 1:​5-​15 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (th phunziro 9)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Sinthani ulaliki wanu kuti ugwirizane ndi nkhani imene mwininyumba watchula, ndipo werengani lemba logwirizana ndi nkhaniyo. (th phunziro 12)

  • Nkhani: (5 min.) w08 7/1 21​—Mutu: N’chifukwa Chiyani Baibulo Limangotchula Mafuko 12 a Isiraeli Pomwe Kwenikweni Anali Mafuko 13? (th phunziro 7)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 57

  • “N’zotheka Kulalikira kwa Aliyense”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Khalani Bwenzi la Yehova​—Muzilalikira Anthu Olankhula Chinenero cha Dziko Lina. Tchulani zina mwa zinthu zomwe zimapezeka mu pulogalamu ya JW Language®.

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia 16:1-9

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 79 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani