Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb21.09 18
  • October 18-24

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 18-24
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21.09 18

October 18-24

YOSWA 12-14

  • Nyimbo Na. 69 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzitumikira Yehova Ndi Mtima Wonse”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Yos 13:2, 5​—Kodi Aisiraeli analandiradi “dziko la Agebala”? (it-1 902-903)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yos 12:7-24 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 6)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale ndipo yambitsani phunziro la Baibulo mu phunziro 01. (th phunziro 20)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 01 mfundo 5 (th phunziro 18)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 84

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • “Muzikumbukira Yehova Nthawi Zonse”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzigwira Ntchito ndi Moyo Wonse Ngati Kuti Mukugwirira Yehova.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs 5:11-17

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 60 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani