September 5-11
1 MAFUMU 9-10
Nyimbo Na. 10 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tizitamanda Yehova Chifukwa ndi Wanzeru”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Mf 10:10, 14—Kodi pali umboni wotani wosonyeza kuti Baibulo silinakokomeze kuchuluka kwa golide amene Mfumu Solomo anali naye? (w08-CN 11/1 22:4-6)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 10:1-13 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba Phunziro la Baibulo—Sl 37:29. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene pa ntchito yapadera yoyambitsa maphunziro a Baibulo. (th phunziro 1)
Ulendo Woyamba: (5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha zimene tinganene pa ntchito yapadera yoyambitsa maphunziro a Baibulo. Kenako yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito phunziro 01 la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Mungapeze Nzeru Zokuthandizani pa JW.ORG”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Limbikitsani omvera kuti azifufuza pa jw.org malangizo a m’Baibulo owathandiza kulimbana ndi mavuto amene amakumana nawo.
Zofunika Pampingo: (7 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 09
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 47 ndi Pemphero